Bambo A Prosper

Bambo A Prosper Where the Past Comes Alive

I like chilling with people, am friendly that's why i opened this forum named "Tiziwe Mbiri za Akatswiri" so that i must have a time to chill with people.

18/09/2025

Akamati UNOFFICIAL RESULTS ndi ulemu chabe koma zimakhala kuti ma results wo ndiwowona ๐Ÿ‘๐Ÿšถ

18/09/2025

2020, zitadziwika kuti Chakwera akutsogola, MDF inayamba kuteteza mavoti. Leronso asilikali atazindikira kuti Daudi Suileman akufuna kusokoneza ma figure, anathamangira ku maofesi a MACRA ndi kuwathamangitsa komanso kutseka ofesi. Ndikunena pano, MDF yayambapo kuteteza mzinda wa Lilongwe.

Tikamati mudya mtoliro mpaka kudziyipitsira mkabudula, it's not a joke. Asilikali omwe aja mumawatuma kupanga zopusa, lero akutembenukirani atazindikira kuti mwaluza.๐Ÿฅด

18/09/2025

๐Ÿคฃ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜ koma uyu abaleee ๐Ÿ™Œ

18/09/2025

Anthu akwiya ndizisankhozi Ase usawaparamule dala ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜๐Ÿคฃ

18/09/2025

Wa Bakili Muluzi TV & Limpopo Fm konzekani kukakhala ma Director a MBC ๐Ÿ™„๐Ÿคญ

18/09/2025

BREAKING NEWZ!

NASA yapanga confirm kuti pofika 2030 dziko lapasi litha kuphulika kuwonjezera ma Continent's ena ndi Nyanja Zina. Akuti chimwala chachikulu chotchedwa Aestroid chathothoka m'malelemu nde anytime chitha kunyenya dziko lapasi. Anthu pafupifupi 50 million atha kuzapselela ndi chiphalaphala chamoto chomwe chili mkati mwa mwalawo.

Kaya tisusa or ayi komano akatswiri azofufuza fufuza ati chimwalachi chikugwela direct ku dziko lapasi kuti chiphwasule mbali Ina ya Earth

Ndikhala ndikusatira mwa chidwi nkhani imeneyi kuti ndidziwe mbari yomwe chizagwere then ndizakuziwisani "Friends of Bambo A Prosper"uti mwina mupange phazi thandize

~Follow @ Bambo A Prosper

18/09/2025

Malawi Elections Updates
As at this hour

At National Level

APM 64%
Chakwera 30.1%

18/09/2025

MZIMU WA SAULOS CHILIMA WATSEKA MAKOMO ONSE OMWE MCP INGADUTSE KUTI ITENGE UTSOGOLERI.

MCP ikufunisitsa kuchitike Re-Run, koma sakuona patsogolo olo dontho chifukwa:๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡

Mzimu wa Saulos Chilima waima njiiii kutseka njira zonse zomwe MCP yakonza kuti idutse kuti ikhale pampando.

Chipani cha UTM chikuswa zedi pa chisankhochi ndipo chikumabwera pa number 3, pena neck to neck ndi MCP. Kutakhala Re-Run ,chipani cha UTM ndichomwe chidzapangitse kuti president wa dziko akhale ndani.

Pa chimenechi, DPP ndiyo idzakwapulenso pachifukwa chakuti mzimu wa Chilima sungalole kuti UTM ipange mgwirizano ndi MCP........UTM idzakumbukira za nkhalango yokhwithima choncho chilakolako chopanga support MCP chidzachokeratu.

~Bambo A Prosper

18/09/2025

If Chakwera win this general elections please someone should take care of my children.
Tell them their father was a good man and he was passionate about things in life.๐Ÿšฎ๐Ÿ˜ญ

18/09/2025

Andale onse ndi akuba komano timaona kuti amene amati akatibela amatisiilako eni akefe Kuti nafenso tinyambiteko๐Ÿ˜‹ Ndiye titakhala tinawona kuti ndi Adad ndi DPP yawo. ๐Ÿ’™๐Ÿ’™๐Ÿ’™๐Ÿ’™๐Ÿ’™

~Good Morning Ma Blues ๐Ÿ’™๐Ÿ’™๐Ÿ’™ Kulikonse Komwe Muli

18/09/2025

Aja a "Boma ๐Ÿ“ Ndilomweri Sitikusintha" aja tabwerani apa ndikuwoneni kenakake ๐Ÿ™„๐Ÿคญ

18/09/2025

NDIKUSAKASAKA ANTHU 338 AWOWO NDIKAWAFUNSE MAGANIZO AWO POMWE ALI.

Mulanje South West Constituency

Lazarus McCathy Chakwera (MCP) 338

Prof. Arthur Peter Mutharika (DPP) 20,281

Address

Ekurhuleni

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Bambo A Prosper posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Bambo A Prosper:

Share