07/10/2025
Kaya amwene Bola Ife tawona basi, tadyesako maso 😬🙄
Komano Guys wait kaye, ndekut tiziwanamiza akaziwa Kuti tili nawo mchikondi kenako kuzawayalusa pamapeto?.
Okay ndi zinthutu zokhudza zachitikazi, munthu kumat uli mchikondi, osadziwa Kuti Chikondi chomwecho pa mawa chikupalamulisa kukuyikisa m'mavuto, tsokadi Poti mulungu anatibisila za mawa. Nthawi zonse ma video otelewa amatumizidwa kweni kweni mukakhala mukunvana anthu awiri ngat okondana kapena kufilana, kaya sindidziwa ngat ena amagulisa ma vídeo otelewa ndilibe umboni kweni kweni.
Koma ndi chipongwe chanji chosungilana mpeni ku mphasa azibambo? munthu wa Mayi kumuyalusa kotele kamba koti chikondi chinatha pakati panu?, this is emotional torture.
To our Sister Small wife, stay strong in these trying and terrible times,dziko ndi limenelo, Lero wachikondi wako,mawa amasanduka m'dani, zinayambila pa Yesu ndi Yudas.
Iliso likhale phunzilo kwa azimayi kapena atsikana, tikakhala mu chikondi tiyeni tiwonesese Kuti zomwe tikumuchitila wa chikondi wathuyo pa mawa zisazatiyike muma Vuto kapena kutiwonongela mbili.
Zikomo ndithu, eeh pepanitu enafe paja kujijilika mwina talowelera nkhani zoti eni ake akudziwana mudziwa paja chikondi ndi anthu awiri🙌🏽, tingoziyang'ana basi tisawonekepo ngati a nzeru apayi, odi basi ndiziwonela nyimbo yanga ya nyuwani ineeee eeh. muyipeza kuma comments mukayifuna. eeeh