CHE NJIMA

Lola pa 12 June, Facebook ikuvuta Vuto si network yanu ai facebook ndiyo ili ndi vuto,  Meta alengeza kuti Facebook, Mes...
12/06/2026

Lola pa 12 June, Facebook ikuvuta
Vuto si network yanu ai facebook ndiyo ili ndi vuto, Meta alengeza kuti Facebook, Messenger ndi Instagram zikukumana ndi mavuto padziko lonse lapansi. Ngati simukutha kulowa kapena ma post sakuwoneka, si foni yanu kapena data yanu ai osasitha password musokoneza zinthu. Osazimisa phone ayi,dekhani ndithu

12/06/2026

Update ya ku Durban Komwe chiwelengelo cha athu chikupitila kukwela

Mtsogoleri wa dziko la South Africa, Cyril Ramaphosa walengeza ndondomeko zomwe boma likhazikitse pofuna kuthana ndi vut...
07/06/2026

Mtsogoleri wa dziko la South Africa, Cyril Ramaphosa walengeza ndondomeko zomwe boma likhazikitse pofuna kuthana ndi vuto la kulowa kwa nzika za maiko ena m'dzikolo mopanda zikalata zoyenera.

Mtsogoleriyu walengeza izi pomwe m'dzikolo mwakhala mukuchitika ziwawa kutsatila kuchuluka kwa mzika za maiko ena.

A Ramaphosa ati boma lawo likhwimitsa malamulo a nthambi yoona zolowa ndi kutuluka pofuna kuthana ndi mchitidwe olowa m'dzikolo mopanda zikalata zoyenera.

Iwo ati boma la South Africa lichilimika pothana ndi katangale komanso ziphuphu ku nthambi yoona za anthu olowa ndi kutuluka pofuna kuonetsetsa kuti amene akulowa m'dzikolo ali ndi zikalata zovomelezeka.

Apa mtsogoleriyu watsindika kuti nthambi za mabwalo a milandu zipitilira kupeleka zilango zokakhala kundende osati kulipilitsa chundapusa pokana kupitilira kulemba ntchito anthu amaiko ena.

Iwo apitilira kulamula nthambi ya apolisi ndi zina kuchita chipikisheni ndi kubweza kwawo anthu onse opanda zikalata zoyenera zokhalira m'dzikolo.

A Ramaphosa alamulanso nthambi zonse zogwira ntchito mmalo wolowera m'dzikolo kulimbikitsa malamulo kwa onse olowa pofuna kuchepetsa mchitidwewu.

Apa mtsogoleriyu watinso boma lake ligwira ntchito limodzi ndi maiko a mu Africa komanso ena onse omwe mzika zawo zimapita m'dziko la South Africa pofuna kugwilana manja poika ndondomeko zothanilana ndi vutoli.

Pomaliza Ramaphosa wadzudzula mzika zadziko la South Africa poyambitsa ziwawa m'dzikolo zokhudza nzika za maiko ena ndipo wachenjeza kuti boma lake sililekerera izi ndipo lithana ndi aliyense wochitila nkhanza mzika iliyonse ya maiko ena.

Wolemba: CHE-NJIMA- Eastern Cape

17/04/2026

BREAKING NEWS,,,

Magesi azima dziko lonse la Malawi lero kuyambila 10:03 am,

Ndipo ESCOM Yasimikiza izi pa tsamba lawo la nchezo

Breaking News Mtsogoleri wa chipani cha Economic Freedom Fighters mdziko la South Africa a Julius Malema, amugamula kuka...
16/04/2026

Breaking News

Mtsogoleri wa chipani cha Economic Freedom Fighters mdziko la South Africa a Julius Malema, amugamula kukakhala ku ndende kwa zaka zisanu, pa mlandu obweretsa chiopsezo poombera mmwamba pa gulu.

Bwalo la milandu kumeneko lapereka chigamulochi lero, m'chaka cha 2018 a Malema adaombera m’mwamba koposa ka 10 monga chisangalalo pa msonkhano wa chipani pomwe padali anthu pafupifupi 20,000.

Koma bwalo la milandu lapereka mwayi kuti a Malema, atha kupanga apilo chigamulocho ku bwalo lalikulu la High Court ngati sadakhutire nacho.

Chithunzi Cha SABC
CHE NJIMA

Iran’s 10 conditions regarding commitments expected from the United States. 1. Non-aggression 2. Continuation of Iran’s ...
08/04/2026

Iran’s 10 conditions regarding commitments expected from the United States.

1. Non-aggression
2. Continuation of Iran’s control over the Strait of Hormuz
3. Acceptance of nuclear enrichment
4. Lifting all primary sanctions
5. Lifting all secondary sanctions
6. Termination of all United Nations Security Council resolutions
7. Termination of all International Atomic Energy Agency Board of Governors resolutions
8. Payment of compensation to Iran
9. Withdrawal of United States combat forces from the region
10. Cessation of war on all fronts, including against the Islamic Resistance of Lebanon

Tivomeleze kuti Iran njadziwindi !

Apa nkumati nkhondo waiwina ndani?BREAKING:🇺🇸🇮🇷🇮🇱 What US and Iran have agreed on:– Iran and the U.S. agreed to a 2-week...
08/04/2026

Apa nkumati nkhondo waiwina ndani?

BREAKING:

🇺🇸🇮🇷🇮🇱 What US and Iran have agreed on:

– Iran and the U.S. agreed to a 2-week ceasefire, in which Israel is also included.
Iran agreed to reopen the Strait of Hormuz during these two weeks.

– In turn, America has agreed to begin negotiations in Islamabad on Friday, based on Iran’s 10-point plan.

– The acceptance of Iran’s 10-point plan, which contains the lifting of sanctions, guarantees of non-aggression, acceptance of nuclear enrichment, formal Iranian control over the Strait of Hormuz and other things, is a precondition for the establishment of a permanent ceasefire.

– If US does not abide by the 10-point plan of Iran, it is likely the war will continue after two weeks.

Welcome Back Bandera wa Chiyawo,,Lero watuluka tsopano ndipo ku Mangochi kwayaka Moto pomwe anthu akukondwelela kutuluts...
02/04/2026

Welcome Back Bandera wa Chiyawo,,

Lero watuluka tsopano ndipo ku Mangochi kwayaka Moto pomwe anthu akukondwelela kutulutsidwa kwake atamaliza chilango chake ,

music is back

31/03/2026

Bwana Dolnad Trump alemba pa tsamba lawo kuti:

Kwa omwe akufuna mafuta akhoza kupita akatenge okha ,ndipo Iwo sakuthandizaso dziko lililonse,,
Akuti aliyese ayendele yake ,ndipo ngati akufuna akhoza kungogula ku America komweko,

Komiti ya National MoonSighting (N-M-C) yomwe imaona za kuoneka kwa mwezi wa Shawwal 1447 wati mweziwu siwunaoke lelo.Iz...
19/03/2026

Komiti ya National MoonSighting (N-M-C) yomwe imaona za kuoneka kwa mwezi wa Shawwal 1447 wati mweziwu siwunaoke lelo.

Izi ndi malinga ndi uthenga womwe komitiyi yatulutsa posachedwa.

N-M-C yati izi zikutanthauza kuti mapemphero a Eid kutsatira kutha kwa nyengo yosala mmwezi wa Ramadan achitika loweruka pa 21 March 2026.

CHE NJIMA

Address

Johannesburg

Telephone

+27718467407

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when CHE NJIMA posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share