Funny video 100%

Funny video 100% Nkhani πŸ”₯

25/08/2026

wagwidwa uhuleπŸ˜‚πŸ€£

Ati khululukani mupase vote  πŸ—³ 2030 ati chakwera anali munthu wabwino kwambiri koma amamusokoneza ndi anthu omuzungulira...
07/08/2026

Ati khululukani mupase vote πŸ—³ 2030 ati chakwera anali munthu wabwino kwambiri koma amamusokoneza ndi anthu omuzungulira 😫

Which uniform is good for school?
02/08/2026

Which uniform is good for school?

Wakumvalira bwino ndiuti apa A or B
01/08/2026

Wakumvalira bwino ndiuti apa A or B

Kwamene muli ndi maso abwino bwino opanda vuto Halland Akumwa chan apa??πŸ€”πŸ€”πŸ€”
01/08/2026

Kwamene muli ndi maso abwino bwino opanda vuto Halland Akumwa chan apa??πŸ€”πŸ€”πŸ€”

Ayihavu nuduziπŸ˜«πŸ˜ƒ
01/08/2026

Ayihavu nuduziπŸ˜«πŸ˜ƒ

Mtsogoleri wa March ndi March Jacinta akufuna kuti anthu onse a Zimbabwe achoke ku South Africa atakana kuchita zionetse...
01/08/2026

Mtsogoleri wa March ndi March Jacinta akufuna kuti anthu onse a Zimbabwe achoke ku South Africa atakana kuchita zionetsero lero pa 31 July 2026.

Anthu a ku Zimbabwe akukonzekera ziwonetsero zotsutsana ndi Purezidenti Mnangagwa atawonjezera nthawi yake yapulezidenti mpaka 2030.

Anthu a ku South Africa adatuluka ndikuchita ziwonetsero mogwirizana ndi anthu a ku Zimbabwe, koma a Zimbabwe omwe ali ku Zimbabwe adatuluka kudzatsutsa.

Jacinta akunena kuti popeza azimbabwe mukukana kuchita zionetsero kapena kuchitapo kanthu ndiye kuti mukusangalala ndi zomwe zikuchitika mdziko lanu ndiye madocuments or no Documents u must go. A Jacinta apempha anthu a ku Zimbabwe kuti azimenyera nkhondo dziko lawo mmalo mokhala amantha ndi kuthawira maiko a anthu ena

Members wa mcp walemba iziπŸ€”πŸ€”πŸ€”πŸ‘‡A Malawi musapuse ndi boma la Dpp chimanga chomwe mukuchiona kutchipa lero lino zonse adas...
01/08/2026

Members wa mcp walemba iziπŸ€”πŸ€”πŸ€”πŸ‘‡
A Malawi musapuse ndi boma la Dpp chimanga chomwe mukuchiona kutchipa lero lino zonse adasayina ndi President Chakwera.

Kuti mudziko lake la Malawi musapezeke munthu wina aliyese ovutika ndi njara ndi chifukwa chomwe adasayina ndi dziko la Zambia kuti agulitsane chimanga chitsika ntengo.

A Malawi ndikufuna kutsimikiza lero lino kunena kuti Dpp momwe ya lowera m'boma palibe chomwe yapanga yikuyendera zomwe Chakwera ndi boma lake la Mcp adasiya .

Palibe ngakhale m'Malawi m'modzi yemwe anganene kuti ankavutika nthawi ya Mcp.
koma zomwe wanena Jersey kabwirazi ndi zoona and a malawi muti naye bwanji uyu????

Small wife Atakhala ndiwo angakhale ndiwo zanji?πŸ˜„
31/07/2026

Small wife Atakhala ndiwo angakhale ndiwo zanji?πŸ˜„

What do you call this?πŸ˜«πŸ˜‚
31/07/2026

What do you call this?πŸ˜«πŸ˜‚

Address

Johannesburg

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Funny video 100% posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share