
20/01/2025
Out now
🚨🚨NEW MUSIC ‼️
"Masiku ano ma artist ambiri kuphatikiza omwe tinkati ndi-a hip-hop akuchulutsa Afro komaso Amapiano kuti atrende. Koma kwa ife hip-hop ndi chi Khalidwe sitingagawukire", Oyimba wa hip-hop, H-One+265 watokotera ma guy onse omwe anathawa hip-hop nkuyamba kuimba zovina ndi cholinga choti a trende.
Iyeyu watulutsa nyimbo yake yotchedwa "Hiphop Sindidzasiya" momwe muli nkhani yonse
Link munsimu 👇🏿