Akadaulo

Akadaulo Entertainment news
(4)

Timachita kufuna kusakhala pabanja tikhozaso kulanda amunanu otengekawo🥰💞
26/08/2026

Timachita kufuna kusakhala pabanja tikhozaso kulanda amunanu otengekawo🥰💞

From inbox 📥 Akuti akugulisa njingayi pamtengo wa 950 sauzande engine yosamasula amene ali serious tipezeni inbox timvan...
25/08/2026

From inbox 📥
Akuti akugulisa njingayi pamtengo wa 950 sauzande engine yosamasula amene ali serious tipezeni inbox timvane

Pheee pamene paja single and happy kubanja tipita koma mochedwa azibambo sakupanganika awa utambwali too much
25/08/2026

Pheee pamene paja single and happy kubanja tipita koma mochedwa azibambo sakupanganika awa utambwali too much

Azibambo lekani kundifusila ku inbox banja likufunika inde koma Azibambo simukhala serious komaso sindikufuna mamuna ame...
24/08/2026

Azibambo lekani kundifusila ku inbox banja likufunika inde koma Azibambo simukhala serious komaso sindikufuna mamuna amene ali kale ndi mwana kwinakwake chifukwa ineso ndilibe mwana ndili ndi zaka 19

Oyela anzanu inu mukuchedwa pati?💝💫🥰👄💋 congratulations 🎊 👏 💐 🥳
23/08/2026

Oyela anzanu inu mukuchedwa pati?💝💫🥰👄💋 congratulations 🎊 👏 💐 🥳

Phee kudikilira zovala ziume tikasake banja🥰 nditakhala chakudya ndikhale chani? 💋
23/08/2026

Phee kudikilira zovala ziume tikasake banja🥰 nditakhala chakudya ndikhale chani? 💋

Ifeso banja timalifuna🥰
22/08/2026

Ifeso banja timalifuna🥰

Congratulations to tiyamike wakwanisa zaka 17 thanks topfan wathu happy birthday 🎂 dear 😘
22/08/2026

Congratulations to tiyamike wakwanisa zaka 17 thanks topfan wathu happy birthday 🎂 dear 😘

😭😭MUBAS STUDENT DIES IN ROAD ACCIDENT💔A first-year, first-semester MUBAS student, Catherine Mvula from Mzimba, has died ...
22/08/2026

😭😭MUBAS STUDENT DIES IN ROAD ACCIDENT💔

A first-year, first-semester MUBAS student, Catherine Mvula from Mzimba, has died after reportedly being hit by a vehicle at Ginery Corner this afternoon in Blantyre.

She was reportedly crossing the road to meet her father, who had travelled from Mzuzu to bring her essential items.

Her body has been taken to the College of Medicine Mortuary.😭😭😭

Our heartfelt condolences go to Catherine’s family, friends, classmates and the entire MUBAS community. May they find strength during this difficult time. May her soul rest in peace. 🕊️

Hello, Akadaulo tapangani postTapanga post fast mkazi uyu sindigona naye tulo timakhala naye ndiwambali zakwathu kuno ko...
22/08/2026

Hello, Akadaulo tapangani post

Tapanga post fast mkazi uyu sindigona naye tulo timakhala naye ndiwambali zakwathu kuno koma ndimachita mantha kuti andikana tamuyankhuleni ndikupasani 50 sauzande kwacha.

Ndamva zambiri za inu akadaulo chonde yesesani

Address

M
Johannesburg

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Akadaulo posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share