Thocco maction Banda

Thocco maction Banda My name is thocco maction Banda

😂😂😂😂 Koma guys iiiii
31/12/2025

😂😂😂😂 Koma guys iiiii

31/12/2025

Lero ndigaweko ndalama Pamudzi pano iiiiiii

Happy birthday to you my dear dad
31/12/2025

Happy birthday to you my dear dad

28/12/2025

For example ex wako Ali ndiukwati ndiye DJ ndiwe ungayambe kuika nyimbo yanji iweyo 😳😳

28/12/2025

Mamuna ofuna banja safuna mkazi kuti uli ndi Ana angt ndiwakalembera ameneyo sichoto azimai ndasikana ukoo 🤣🤣

28/12/2025

2026 ndikufuna adani anyowani akale mwatha phavu

28/12/2025

Chaka ndiye chikupita kumapeto ichi alipo Ali ndi funso or dandaulo 🙄

28/12/2025

Mkazi anakusiyani chifukwa chosowa ndalama apa muli busy kusaka mkazi wina Malo mosaka ndalama tazikulan achimwen

27/12/2025

Bola amene mwatenga m'mimbanu kubeleka ndi September koma matenda eee 😂😂😂😂

Muthu ukakhala ndi ndalama uzipanga zitukuko kwanu osati nziko ya weni Taonani Napoloyo zombe akumanga company yopanga f...
27/12/2025

Muthu ukakhala ndi ndalama uzipanga zitukuko kwanu osati nziko ya weni Taonani Napoloyo zombe akumanga company yopanga feteleza kuno kwathu ku malawi company ikumangidwa ku Dowa ndipo akuti iyamba kugwila ntchito chaka cha mmawa mwedzi wa April congratulations Mr zombe

27/12/2025

Pakubwera pa 31 mukaonjezere matenda mwatenga pa 24 ndipa 25 aja agalu inu

Address

15 Glencoe Road
Johannesburg

Telephone

+27634752198

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Thocco maction Banda posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share