Leezer dada

Leezer dada Fashion designer 🩱
Musician🎵🎤
CEO ,of elzeer .clothing brand
Content creator
Tailor ✂️🪡
(2)

22/08/2026
22/08/2026

Muli bwanj nose kumene muli ? Ndikukhazikisa program yotchedwa soulmate wanga♥️ program yi idzapangidwa lounch pa 24 august 2026

KODI PROGRAM YO NDIYOTI CHANI?
(1) in simple way tingoti kulumukizisa athu kuti apeze wachikondi kudzela mwa ine leezer dada

KODI MUDZIPELEKA CONNECTION YO DZIKO LOSE?
(1) pakali pano zizichita ku South Africa 🇿🇦 kokha

NANGA KUSUNGA CHISISI ZIDZIKHALA MOTANI?
(1) ndipo palibe amene azidziwa kuti inu mukufuna mwamuna or nkaz kupatula ine ndi inu
(2)ndipeleka whatsapp number imene muthu azitumiza information yake then soulmate wake akapezeka azipasidwa mwayi kamodzi basi ngat zavuta basi
(3)osatumuza hi ayi just go straight to the point pamene ukutumiza information yako ku watsapp ine ndizabisa chisisi moopa mulungu komaso as kulemekeza tchito yanga

KODI MUZIPANGA ULELE
(1) yama data nanga tizitenga kuti🥹
Pa connection fee iliyose tizifuna 50 Rand imene izitumizidwa ngati voucher

KODI GANIZO LIMENELO LABWELA CHIFUKWA CHANI
(1) athu ambili ku South Africa 🇿🇦 amakhala single kwambili ena kuno anabwelela kuzasaka mabanja ena kuzapeza mwamuna ena kuzapeza nkazi
Ena kungofuna kuti azingochosana chilakolako ena kupezelapo thandizo

Tidzilowalowa live pa tiktok pa week kawili
After zikayambika komaso tidzipanga post pa facebook p***a almost everyday

Onyoza salephela komaso ophwekesa

NDATHA INE WANU Leezer dada

22/08/2026

Program ndiyomwe ija yotchedwa soulmate wanga🌺

wanga

Send a message to learn more

22/08/2026

Program ndiyomwe ija yotchedwa soulmate wanga♥️

Alamu anu
21/08/2026

Alamu anu

Chiliza cha legend rucias bandaKeep resting in peace ✌️
21/08/2026

Chiliza cha legend rucias banda

Keep resting in peace ✌️

Address

Johannesburg

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Leezer dada posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share