Malawi news update

Malawi news update Malawi news update and entertainment
(3)

KatunduMr Norman chisale awalonjeza Anthu akudera lawo kuti asazalipilenso ma bill amipope. Achisale ati iwowo ndi amene...
31/08/2026

Katundu

Mr Norman chisale awalonjeza Anthu akudera lawo kuti asazalipilenso ma bill amipope. Achisale ati iwowo ndi amene azilipila ma bill onse

MP wa Kwanuko akupanga chani ?

31/08/2026

Anthu mu Lilongwe muno akuti chipani cha MCP chithesedwe apange China

31/08/2026

APM earned his masters degree 60 years ago. Koma agogo anu amati kale Anthu ankalekezera 8

31/08/2026

HON. moses kunkuyu ndi DR. Lazarus Chakwera akukana kukawonekera ku commit yomwe ikufufuza zangozi yandege

Apolice amanga Mkulu wakale wa bungwe la mera bambo collings magalasiZikumveka kuti awamanga kamba kokhuzidwa nawo kuti ...
31/08/2026

Apolice amanga Mkulu wakale wa bungwe la mera bambo collings magalasi

Zikumveka kuti awamanga kamba kokhuzidwa nawo kuti anadya dolla za amalesi hotel

31/08/2026

Amupwetekanso uku

Full time

Ekhaya youth 2 : manoma youth 1

Malawi news update here to confirmTeam ya manoma yasankha Patrick mabedi ngati head coach ogwilizila malo mwa bobo mping...
31/08/2026

Malawi news update here to confirm

Team ya manoma yasankha Patrick mabedi ngati head coach ogwilizila malo mwa bobo mpinganjira yemwe amuyimika mawola ochepa apitawa

Mabedi akhale agwila limodzi ndi nginde

Bungwe la FAM yasankha Bobo mpinganjira kukhala head coach wa Malawi u23 nation teamTeam ya malaw u23 ikhale ikusewera m...
31/08/2026

Bungwe la FAM yasankha Bobo mpinganjira kukhala head coach wa Malawi u23 nation team

Team ya malaw u23 ikhale ikusewera ma game African cup qualifies mwezi uno

Congratulation coach bob mpinganjira

Ine ngati admin wa manoma Paganizo yomuchosa bobo ineyo  sindikugwilizana nazo ndithu kapena masapota anzanga mukugwiliz...
31/08/2026

Ine ngati admin wa manoma

Paganizo yomuchosa bobo ineyo sindikugwilizana nazo ndithu kapena masapota anzanga mukugwilizana nazo?

Nanga game ili pa 6 atinyamule ndani poti timadalila bobo?

Team ya Wanderers yayamba yaimitsa kaye  ntchito (Suspension) coach wake Bob mpinganjira .Wachiyao Bulasa
31/08/2026

Team ya Wanderers yayamba yaimitsa kaye ntchito (Suspension) coach wake Bob mpinganjira .

Wachiyao Bulasa

Address

Johannesburg

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Malawi news update posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share