Vincent Chitemango Mr udongu

Vincent Chitemango Mr udongu Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Vincent Chitemango Mr udongu, Digital creator, 13 le cateau Road, Johannesburg.
(1)

YESAYA 12 : 2 Taonani, Mulungu ndiye chipulumutso changa; ndidzakhulupirira, sindidzaopa; pakuti Yehova Mwini ndiye mphamvu yanga ndi nyimbo yanga, Iye ndiye chipulumutso changa.

15/09/2026
16/06/2026

mulungu alemekezeke chifukwa cha zabwino zonse zimene amatichitila tsiku ndi tsiku

YESAYA 61 : 1 Mzimu wa Ambuye Yehova uli pa ine; pakuti Yehova wandidzoza ine ndilalikire mau abwino kwa ofatsa; Iye wan...
02/06/2026

YESAYA 61 : 1 Mzimu wa Ambuye Yehova uli pa ine; pakuti Yehova wandidzoza ine ndilalikire mau abwino kwa ofatsa; Iye wanditumiza ndikamange osweka mtima, ndikalalikire kwa am'nsinga mamasulidwe, ndi kwa omangidwa kutsegulidwa kwa m'ndende;

Kusowa Kwa ntchito matenda osiyana siyana mumasulidwe mudzina la ambuye wathu mulungu wakumwamba amen ๐Ÿ™ ๐Ÿ™

Koma wina wa inu ikamsowa nzeru, apemphe kwa Mulungu, amene apatsa kwa onse modzala manja, niwosatonza; ndipo adzampatsa...
30/05/2026

Koma wina wa inu ikamsowa nzeru, apemphe kwa Mulungu, amene apatsa kwa onse modzala manja, niwosatonza; ndipo adzampatsa iye.

Kodi inu ndine tikusowa chiyani Kuti timupemphe mulungu atichitile chimene tichisowa tiyani timuwuze mulungu chimene tichifuna amen ๐Ÿ™ ๐Ÿ™

Mukhale ndine dzuwa lalowa, Wagwa usiku bwenzi lisowa,Ndilibe wina wondithandiza, Wa mphamvu ndinu, mkhale ndinetu.Mulun...
28/05/2026

Mukhale ndine dzuwa lalowa, Wagwa usiku bwenzi lisowa,
Ndilibe wina wondithandiza, Wa mphamvu ndinu, mkhale ndinetu.
Mulungu alemekezeke chifukwa cha zabwino zonse zimene amatichitila tsiku ndi tsiku

Ngati mwaona zisomo chikondi cha mulungu chikuchitika pamoyo wanu Lero ingonenani amen ๐Ÿ™

MIYAMBO 10 : 4Wochita ndi dzanja laulesi amasauka;koma dzanja la akhama lilemeretsa.Koma inu ndi ine timalimbikila kugwi...
23/05/2026

MIYAMBO 10 : 4
Wochita ndi dzanja laulesi amasauka;koma dzanja la akhama lilemeretsa.

Koma inu ndi ine timalimbikila kugwila ntchito usana ndi usiku Koma sitikuchita bwino, sizoti ndife aulesi ayi koma tiyeni timuuze Mulungu atichitile Chifundo Kuti adalitse tchito zathu Kuti kuyamba lelo tisakhale Ngati awulesi

Mulungu andalitse ntchito zimene tikugwila amen ๐Ÿ™

AROMA 2 : 11For there is no partiality with God.pakuti Mulungu alibe tsankho.Mulungu amakonda aliyense posatengela machi...
22/05/2026

AROMA 2 : 11
For there is no partiality with God.

pakuti Mulungu alibe tsankho.

Mulungu amakonda aliyense posatengela machimo anthu ndi chifukwa chake inu ndine tili ndi Moyo lero lino mulungu alemekedzeke chifukwa cha mau awa amen ๐Ÿ™

Mulungu akundalitseni

Mulungu amagwilitsa ntchito zimene tili nazo Kuti tipeze zimene tilibe mwachisazo mulungu watipasa zipatso Koma ndalama ...
22/05/2026

Mulungu amagwilitsa ntchito zimene tili nazo Kuti tipeze zimene tilibe

mwachisazo mulungu watipasa zipatso Koma ndalama tilibe zofunika kungulitsa zipatso Kuti tipeze ndalama inu ndine mulungu watipasa Nzeru Kuti tipeze zimene tilibe.
chonde pangani follow like and comment

Kodi mumaziwa Kuti zochepa zimene inu ndine tili nazo ndindalitso Kwa anthu ena?? Ena akupemphera usana ndi usiku Kuti a...
21/05/2026

Kodi mumaziwa Kuti zochepa zimene inu ndine tili nazo ndindalitso Kwa anthu ena??
Ena akupemphera usana ndi usiku Kuti apeze zimene inu ndine tili nazo Koma inu ndine sitiyamika nazo mulungu chifukwa tikuti ndizochepa pamene, ena akusowa mphamvu zimene inu ndine tili nazo Koma inu ndine sitilemekeza nazo yehova mulungu okhala kumwamba, inu ndine tikundandaula Kuti lero tadya masamba Koma pamene alipo ena lero sanadye ndikomwe๐Ÿฅฒ

Mulungu atichitile Chifundo Kuti kuyamba lero tiziyamika pazabwino zimene watichitila amen ๐Ÿ™

pangani follow

Masalimo 14 : 1Wauchitsiru Amati mumtima mwake, kulibe Mulungu. achita zovunda, achita ntchito zonyasa; kulibe wakuchita...
21/05/2026

Masalimo 14 : 1
Wauchitsiru Amati mumtima mwake, kulibe Mulungu. achita zovunda, achita ntchito zonyasa; kulibe wakuchita bwino.

Kodi inu ndine timati chani mumtima mwathu mulungu atichitile Chifundo ๐Ÿ™

Psalm 14 : 1
The fool has said in his heart, โ€œThere is no God.โ€ They are corrupt. They have done abominable deeds. There is no one who does good.

Address

13 Le Cateau Road
Johannesburg

Telephone

+27677353975

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Vincent Chitemango Mr udongu posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Vincent Chitemango Mr udongu:

Shortcuts

Share