CHE NJIMA

19/06/2025



National mourning ya former president waku Zambia Late Edgar Chagwa Lungu yathetsedwa.

President wa ku Zambia Hakainde Hichilema HH wathedtsa kuti pasakhaleso holiday yomwe anakhazikitsa kuti alire maliro a former president yu pomwe pangodutsa 14 days chimwalilireni ku South Africa, president yu wapanga izi chifukwa cha kusamvana ndi aku banja la former president.

Zambiri zili mu video iyi👇

Israel-Iran updates Britain just now 10 minutes ago yaitanisa emergency meeting  muchipinda Chao chotchedwa COBRA.  ( Ca...
18/06/2025

Israel-Iran updates

Britain just now 10 minutes ago yaitanisa emergency meeting muchipinda Chao chotchedwa COBRA. ( Cabinet Office Briefing Room A) Akukumana kupanga chiganizo za nkhondo ya Iran- Israel .

Iwo Akukumana Russia itangopeleka Warning kwa USA kuti isalowele nkhondo.

UK prime minister will chair the meeting apapa wapanga Land kumene from G7 Meeting Ku Canada sanapume akupite straight mu COBRA room

Will update

18/06/2025

Akamati kungwa m'chikondi amanena izi

17/06/2025

Athu aku Machinga akwiya now Atupele Muluzi 😳


Anthu omwe amachita business yo order katundu kunja kwa dziko lino akonza ma Demo lachinayi likubwelari pa 19 June pofun...
17/06/2025

Anthu omwe amachita business yo order katundu kunja kwa dziko lino akonza ma Demo lachinayi likubwelari pa 19 June pofuna kuwonesa mkwiyo wawo pakusowa kwa Forex m’dziko muno.

atopa ndi black market akuti ikuwasokoneza malonda awo nde akufuna akakumane ndi adindo face to face akatule nkhawa zawo. a DC apereka kale chilorezo kuti anthuwa apitilire ndi Mademo awo

17/06/2025

Iran - Israel updates

35 minutes ago Israel yatumiza uthenga kwa Supreme leader ndikumuuza kuti Uonere imfa ya Saddam Hussein iwenso zikhala chimodzi modzi usakaike

Watumiza uthengau ndi minister of Defence wa Israel Katz

In his words " Remember what happened to your fellow Dictator in Iraq who took the path against Israel"

Will update

Israel -Iran update Foreign Affairs minister wa Iran wanena kuti Donald Trump asadikile kuti akambilane week yamawa . He...
17/06/2025

Israel -Iran update

Foreign Affairs minister wa Iran wanena kuti Donald Trump asadikile kuti akambilane week yamawa . He can just make one phone call Ku Israel and nkhondo ikhoza kutha .

Trump is proposing kuti akambilane week yamawa chifukwa panopa akuti akutsegula company ya phone yake . Mtolankhani anamufunsa kuti ndiye zikugwirizana bwanji iye wayankha kuti zonse nzofunika

Donald Trump akhala akuyendesa wrestling WWE kwakanthawi , Amagwiranso ntchito kwa Mike Tyson pa nkhonya komanso sajomba kumasewera a nkhonya a UFC

Sabata yatha anatuluka mu meeting yofunika kwambiri ndikukaonelela nkhonya ya UFC . Anakhala mpando wakutsogolo ndikutenga ma glovo a osewerawo atamaliza

" I told him to sign the deal he refused so perhaps next week we will see "

17/06/2025



Apolisi ku Ndirande ati nzimayi wa zaka 37 wafa ndipo ena asanu avulala kutsatira ngozi ya galimoto yomwe yachitika mumsewu wa Sanders pa 16 June munzinda wa Blantyre.

Mneneri wa polisi ya Ndirande Chibisa Mulimbika wati ngoziyi yachitika nthawi ya 16:30 pomwe dalaivala wa galimoto ya mtundu wa Iveco Trakker tanker PE 1244 dzina lake Gift Malata wa zaka 42 analephera kuwongolera komanso kulephera kuima ndipo anakaomba galimoto ya mtundu wa Hino Dutro Light Lorry NS 5824 yomwe imayendetsa ndi Collins Galeta wa zaka 25 ndipo inanyamula anthu asanu ndi modzi.

Chibisa wati anthuwa(6) anathamangira nawo kuchipatala cha gulupu komwe asanu anawathandiza(outpatients) ndipo m'modzi yemwe dzina lake ndi Nelia Njobvu wamwalira atangofika pa chipatalachi.

Malemuwa amachokera m'mudzi mwa Chekimu mfumu yaikulu Nsomba mu nzinda wa Blantyre.

  front page: United Democratic Front (UDF) leader Atupele Muluzi has asked Democratic Progressive Party (DPP) president...
17/06/2025

front page: United Democratic Front (UDF) leader Atupele Muluzi has asked Democratic Progressive Party (DPP) presidential aspirant Peter Mutharika (APM) not to contest in the September 16 Presidential Election, claiming that he is old and should rest.

Breaking news Former Zambian President Edgar Lungu has died in South Africa.Zambia's Diamond TV reports that Lungu was t...
05/06/2025

Breaking news

Former Zambian President Edgar Lungu has died in South Africa.

Zambia's Diamond TV reports that Lungu was this morning at a hospital for a routine review but later developed chest complications.

The family and the state have yet to make statements.

He was 68 years old.

Ndiy kunali  ching'oma  amalemu aluso, izi ndi  10 mwa nyimbo zake zomwe zinabemba thawi imeneyooo   Link mu comment sec...
24/05/2025

Ndiy kunali ching'oma amalemu aluso, izi ndi 10 mwa nyimbo zake zomwe zinabemba thawi imeneyooo Link mu comment section 👇🎶

ching'oma

Address

Kensington

Telephone

+27718467407

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when CHE NJIMA posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share