Nsamala TV

Nsamala TV Nsamala TV is a page that bring you to the truth and deliverance

11/08/2026

Koma anawa kkkk

11/08/2026
10/07/2026

Mudzi mwina ku France zaka za pakanthawi kunali chikhalidwe chochititsa chidwi.

Amati munthu ukakwatira kapena kukwatiwa tsiku lililonse mamawa mu chakudya chamamawa amaikamo poison ... Izizi zimachitika kwa amuna okhaokha ,kotero azimai mamuna WAWO akamapita kaya ku ntchito kaya kocheza amaonesesa kuti amuthilira chiphe mu chakudya chamamawa.

Mankhwalawo anali ogwira ntchito thupi mwa munthu kwa maola 8 ndipo mukangofikira maola 10 usanafike pankhomo zimakuvuta .

Cholinga cha mankhwalawa amafuna mamuna akachoka azibwera pa nkhomo mwacangu chifukwa ikangokwana maola 8 uli koyenda usanafike kunyumba umadwalika mwina mpaka kufa ndipo amuna ambiri poopa kufa amabwera kunyumba maola 8 asanakwane chifukwa ukafika kunyumba amakupasaso chakudya chomwe mumakhala mankhwala osulusa poison uja ..

Izizi zinapangisa azibambo ambiri kukhala okhulupilika mayendedwe mwai ndipo anasitha miyoyo yawo yokhala odalilika pa nkhomo pawo ..

Pokutha panthawi azibambo anayamba nawoso kumawathilira azikazi awo chimodzi modzi ndi cholinga CHOTI pasamakhale kukaikilana.

🤗😟Mukudziona bwanji ? Izi zinali nkhaza kapena zabwino?

Baibulo limatiphunzisa kunena kapena kupanga chilungamo .... Choncho chilungamo sichituluka chifukwa chakubanika aiii koma chilungamo chichokera mkamwa molungama.

Tsiku labwino

Lucius Joseph
Mtukanika Junior
Nsamala TV

10/07/2026

Okumva wamva

05/07/2026

Ndili ndi amuna awiri akufuna atsikana awiri ku Blantyre. Mkhale ma Uni students

Aliyense akapasidwa K150,000.00

0987869558

05/07/2026

Once you lie to me😭🥹

Lucius Joseph

04/07/2026

Tipangeni follow kuti izi zisakuphonyeni

04/07/2026

Mulibwanji

Ndimafuna mudziwe kuti chikondi si pakamwa koma zomwe ukupanga .... Okondeka anuwo alichoncho chifukwa cha inu ...

Mawa muzawalira....😭Kumaliopa mawa.

24/06/2026

Mwamuna wa mwiniyo
Atangomulandira yesu
Sibasi asisi kudula kukhala komweko?

Address

Midway
Middelburg

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Nsamala TV posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share