Nkhani Za Jozi

Nkhani Za Jozi Nkhani pa Jozi yimakupasirani nkhani zoona zokha zokha dziko lonse la south Africa popanda matha ndi

Nkhani za Jozi siyiremba nkhani kopanda umboni , tili pano kukupasilani nkhani zoona zokha zokha zomwe zikuchitika kuno ku South Africa.

Njala yavuta ku south Africa pamene nkazi wina wapanga post ku page yake ndipo walemba kuti .. nthandizeni yaufa kupakul...
20/02/2025

Njala yavuta ku south Africa pamene nkazi wina wapanga post ku page yake ndipo walemba kuti .. nthandizeni yaufa kupakula kulipo zambiri mu comment

Nkhani yangotipeza kumeneSanaphedye yinali vuto la phone
20/02/2025

Nkhani yangotipeza kumene
Sanaphedye yinali vuto la phone

HELLO ABALE NDI ALONGO MUNTHU UYU WAPHEDWA KUNO KU SOUTH AFRICA LERO PA  19 FEBRUARY 2025 KAMBA KA NKAZI WAMWINI KOMA AB...
20/02/2025

HELLO ABALE NDI ALONGO MUNTHU UYU WAPHEDWA KUNO KU SOUTH AFRICA LERO PA 19 FEBRUARY 2025 KAMBA KA NKAZI WAMWINI KOMA ABALE AKE SAKUZIWIKA CHONDE TUMIZANI KUMA GROUP ENA MWINA ABALE AKE NKUZIWIKAKO ZIKOMO

STRANDED IN JOBURG  [ From the inbox 📥]Pali munthu dzina lake ndi Rajab Akim, wachokera ku Zomba ku ndege, wafika kuno k...
18/02/2025

STRANDED IN JOBURG [ From the inbox 📥]

Pali munthu dzina lake ndi Rajab Akim, wachokera ku Zomba ku ndege, wafika kuno ku brakpan joz, ati akufuna Peter Phiri emwe phone yake siikutheka.

Munthuyu ali stranded chifukwa alibe kokhala ndiye please tatithandiziren kupeza abale ake ku malawi ko or kunoko Ma number anga ndi +27670717448 or
+27693403848

15/02/2025

Tsikana osayakhula wapezeka ku south Africa

15/02/2025

Nkhani zophedwa mu January 2025 south Africa

15/02/2025

Nkhani a atsikana awiri omwe you anaba ndalama ku south Africa inayamba chonchocho... Chigawo choyamba

15/02/2025

Mumalawawi anasowa ku south Africa zambiri mu video

02/10/2024

Tilandileni

Address

Muldersdrift

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Nkhani Za Jozi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share