Deejay Fix

Deejay Fix Artist/song writter &Club DJ
(21)

This is the pic I took before the video
11/12/2025

This is the pic I took before the video

11/12/2025

I was driving somewhere passing this place, then I fell in love with the flowers.

Ma managers achimuna don't marry,coz kafukufuku akuwonesa k*t ma boss lady wa amafuna single men to manage them 🤣🤣ukango...
11/12/2025

Ma managers achimuna don't marry,coz kafukufuku akuwonesa k*t ma boss lady wa amafuna single men to manage them 🤣🤣ukangokwatila mbola🤣🤣 .
Zinayambila ku khameri so we can conclude that the history has repeated its self

11/12/2025

Apa sizinayende, RIP auntie

Bring death sentence back ,this nonsense will stop
11/12/2025

Bring death sentence back ,this nonsense will stop


Apolisi ku Lilongwe amanga a Limbanazo Chikalipo azaka 20, powaganizira k*ti anapha ogwira ntchito pa chipatala cha Partners in Hope, a Peter Mzungu azaka 50.

Malingana ndi mneneli wa polisi ya Lilongwe a Hastings Chigalu, apolisi apezaso laptop ya Lenovo, chikwama cha laptop-yo komanso katundu wina yemwe anabedwa pa nthawi yomwe a Mzungu adachitidwa chipongwe.

A Chigalu ati, potsatira za chiwembu zomwe zinachitikira a Mzungu pa 27 November, apolisi anakhazikitsa kafukufuku wawo yemwe anawatengera kwa a Blessings Chitukula azaka 19, komanso a Medson Nackyon azaka 35.

Awiriwa ak*ti anapezeka ndi katundu yemwe anabedwa tsiku lomwe a Mzungu anachitilidwa chiwembu, ndipo, apolisi atawafunsa komwe anatenga katunduyi, ak*ti anawulula k*ti anagula kwa a Limbanazo Chikalipo.

A Chigalu ati, apolisi atamanga a Chikalipo, awulula k*ti anaba katunduyi kwa a Mzungu atawamenya ndi chitsulo m'mutu. A Peter Mzungu omwe amkagwira ntchito ngati owerengera chuma kuchipatala cha Partners in Hope, anamwalira pa 1 December akulandira thandizo pachipatala pomwepa.

(by Innocent Kumchedwa -Lilongwe:12/12/25)

Tinali onenepatu ife koma zomwez izi eeeish
11/12/2025

Tinali onenepatu ife koma zomwez izi eeeish

Masiku amenewo
11/12/2025

Masiku amenewo

11/12/2025

Zinthuzi pena pake sizifunika maturity

History ya ku Khameri has reapted itself 🤣🤣.Ma managers musamakwatile for own safety.
11/12/2025

History ya ku Khameri has reapted itself 🤣🤣.Ma managers musamakwatile for own safety.

Facebook itiwonesa zinthu🤣🤣
11/12/2025

Facebook itiwonesa zinthu🤣🤣

11/12/2025

The only thing I can afford for Christmas this year is to pray for y'all🤦🤣

10/12/2025

Mwati nkhani ili apa nja njoka di koma��

Address

Kranshoek Du Plessis
Plettenberg Bay
6600

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Deejay Fix posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Deejay Fix:

Share