Dister broh mawilloh

Dister broh mawilloh chilling and updating each other things that happens surround area

12/09/2025

Kukasungu kukhala ndi Bluetooth speaker ndwe bwana wamkulu

12/09/2025

Nthawi zino wangongole kuimba video call ine ndayidula kenako ndalemba k*t boss ndili offline 🤪

12/09/2025

Mkusapota chipani chiti inu ku bedroom window katan MCP sitting room DPP ku toilet pp bathroom odya zake alibe mlandu

12/09/2025

Ndi azibambo ochepa kwambili angathe kucheza ndimkaz nthawi yayitali osamufusila ndilipo ndekha 🤪

12/09/2025

Ndi president uti amene vote yanu azayivera fungo lokha

11/09/2025

Pena manyazi amakugwira k*t walemba status yojeda nde munthuyo osayiona mpakana kupanga disappear

11/09/2025

Kale kunalibe ma bathing towels nde kunali kuponyana mumwambatu mpaka uume 🤣

11/09/2025

Ndek*t nonse muli offline ndilipo ndekha

11/09/2025

Ak*ti inde kujoni mkuphunzira chizungu while mkulandila ndalama koma chizungu chanu ku Malawi simungalankhule pa meeting 😩😩

11/09/2025

Mau oti boma ndilomweli pa ground sunganene atha kukuponda mpaka no ma ARVs 😩

Ak*t muzipatala zaboma ma ARVs achepa china kumakavoterabe chakwera koma chili positive tikuonda tili pa dosage kuli bwa...
10/09/2025

Ak*t muzipatala zaboma ma ARVs achepa china kumakavoterabe chakwera koma chili positive tikuonda tili pa dosage kuli bwanji k*t tikhale popanda dosage ambuye please mankhwala awa afike mpaka ena abwere 😩😩

10/09/2025

Ukapezeka ndi malaria amalemba zoti sungawerenge pezeka ndi edzi uone capital letters

Address

Chelsea Road
Port Elizabeth Sp

Opening Hours

Monday 09:00 - 17:00
Tuesday 09:00 - 17:00
Wednesday 09:00 - 17:00
Thursday 09:00 - 17:00
Friday 09:00 - 17:00

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Dister broh mawilloh posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share