Concerned Citizens

Concerned Citizens Our aim is to end corruptions in our beloved country (Malawi)

12/01/2025

Chimwendo Banda kudya misonkho yathu, amalawi tidalakwanji

Vp agonanso pa cement lero
12/01/2025

Vp agonanso pa cement lero

  wakana nyasi
04/04/2022

wakana nyasi

Timadziwa ife, iyi sinkhani yochita kufunsa ayi.Uyu akusokoneza chipani cha DPP
17/03/2022

Timadziwa ife, iyi sinkhani yochita kufunsa ayi.

Uyu akusokoneza chipani cha DPP

  pa chithandizo chanu koma chabwera mochedwa😓Atumizireni amalawi omwe ali ku Ukraine aja, chithabdizo achipeza tsopano ...
28/02/2022

pa chithandizo chanu koma chabwera mochedwa😓

Atumizireni amalawi omwe ali ku Ukraine aja, chithabdizo achipeza tsopano komabe dziko lathu lachedwa nazo izi

Mmmmmm Russia ndi nkhani zina.Moti dzuro laliwisili anatseka njira zonse za mlengalenga kuti mudziko lawo kumanso mayiko...
25/02/2022

Mmmmmm Russia ndi nkhani zina.

Moti dzuro laliwisili anatseka njira zonse za mlengalenga kuti mudziko lawo kumanso mayiko ena oyandikirana nawo kusadutse ndege ina iliyonse

President wa dziko la Senegal walamura kuti lero lolemba mudzikomo mukhale holiday pofuna kusangalal mokwanira ndi kupam...
07/02/2022

President wa dziko la Senegal walamura kuti lero lolemba mudzikomo mukhale holiday pofuna kusangalal mokwanira ndi kupambana kwa timu ya mdzikoli mumpikitsano uja wa maiko onse amuno mu africa

Golden boot winner, player of the tournament and goalkeeper of the tournament
07/02/2022

Golden boot winner, player of the tournament and goalkeeper of the tournament

Mwalimbama nako kulimbana kwabwino
06/02/2022

Mwalimbama nako kulimbana kwabwino

06/02/2022

Mmene mphoto zayendera ku mpikisano wa afcon.

Champions: Senegal

Runners up: Egypt

Third place: Cameroon

Fourth place: Bukina Faso.

Individual Awards

Player of the Tournament: Sadio Mane

Best Goalkeeper: E. Mendy

Top Goal Scorer: Vincent Aboubakar

06/02/2022

Congratulations Senegalese for being champions of 2021 Afcon

Malawi ikupita patali ndithu
06/02/2022

Malawi ikupita patali ndithu

Jordanian football club Al Hussein Irbid SC has signed Flames and Civil United lofty defender Lawrence Chaziya.

The outfit has since officially posted about centre-back on their page.

The club, based in Irbid, competes in the Western Asian country's top-flight league.

Chaziya was among the most outstanding players for the Malawi football national team at the just ended 33rd edition of TotalEnergies African Cup of Nations (Afcon) finals in Cameroon.

(Report by Solomon Manda)

04/02/2022

Thom Mpinhanjira.

Bwalo lalikulu la supreme court, lero lapereka bail kwa Thomson Mpinganjira yemwe adamangidwa chaka chatha pa mlandu wofuna kupereka ziphuphu kwa ma judge omwe amkamva mlandu wa zisankho za 2019.

Mulungu alinafe ndithu, lero mabwalo athu awonetserako pang'ono kuti iwo ndi woyima pawokha osati kutumidwa ndi boma lolamura

ZampiraTimu ya mpora wa miyendo koma osewera ake ndi azimayi yomwe inkatchedwa kuti Blantyre Zero tsopano yagulidwa ndi ...
03/02/2022

Zampira

Timu ya mpora wa miyendo koma osewera ake ndi azimayi yomwe inkatchedwa kuti Blantyre Zero tsopano yagulidwa ndi Timu ya nyasa Big Bullets ndipo izitchedwa Nyasa Big Bullets womens Club, izitu zili chomwechi chifukwa cha malamuro omwe Caf yayika oti timu yomwe izipikitsana nawo mu mpikinsano wa africa confederation Cup izilhala ndi timu ya mpira wa miyendo koma osewera ake ali azimayi.

Zabwino zonse maule

Thursday, February 3, 2022

Club Statement: Acquisition of Blantyre Zero Women’s FC

Nyasa Big Bullets Football Club can confirm the acquisition of Blantyre Zero Women's Football Club.

Following the Board’s approval and completion of the acquisition, the team is with effect from 1st February 2022 known as Nyasa Big Bullets Women's Football Team.

This is in line with the Club Licensing System requirements and one condition for African teams to participate in the Confederation of African Football Champions League as resolved by the CAF Executive Committee in 2021.

“We are welcoming a new product on board and we believe Bullets will build a solid women’s team that will strongly compete at national level and be able to participate in regional and continental competitions,” says Nyasa Big Bullets chief executive officer, Suzgo Nyirenda.

The Club now has four teams to its name; Nyasa Big Bullets Senior Team, Nyasa Big Bullets Reserves, Nyasa Big Bullets Youth and Nyasa Big Bullets Women’s Team.

Nyasa Big Bullets FC.

Zikumveka ngat zabwinotu
01/02/2022

Zikumveka ngat zabwinotu

Football Association of Malawi (FAM) lapanga ubale ndi bungwe laku France lotchedwa Royal Soccer Scout Firm kuti lithandizire kugulisa osewera a mdziko muno ku Ulaya🗣️

29/01/2022

Zomwe tachitako kuchilendo kuja

Nduna zija amaliza kuzisankha ndipo zonse pamodz zilipo 29
28/01/2022

Nduna zija amaliza kuzisankha ndipo zonse pamodz zilipo 29

Address

Pretoria

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Concerned Citizens posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Concerned Citizens:

Share