Malawi Trends TV

Malawi Trends TV Kubweletsa nkhani zochitika
(3)

14/07/2026

Please please musiyeni Young Machine awuse mu mtendere🕊️🕊️

Mwaona zomwe anthuwa ayamba kupanga zokhudza Bolo Young Machine💔💔

MTTV
14/07/2026

14/07/2026

Zathera misozi m'boma la Balaka ku bwalo la milandu, koki mudakakhala judge mudakatani pa nkhaniyi?

MTTV
14/07/2026

14/07/2026

Zoopsa m'boma la Mzimba💔😭😭

Nkhuku idasokoneza mwambo wa maliro a nkulu wina kumeneko ali kumanda.

MTTV
14/07/2026

13/07/2026

Ena simunayitsate,

Nkangano wa dziko la Malawi ndi Tanzania zakhala motere kuti ziyambike.

MTTV
13/07/2026

13/07/2026

Nkhani ya nzibambo amene wamangidwa kamba kochinda(kunyenga) azikazi aweni mokakamiza nkumawanamiza kuti iyeyo ndi msilikali wa m'boma la Nkhatabay.

MTTV
13/07/2026

13/07/2026

M'mene nkhondo idaliriri lero kwa Chinsapo 2 mu mzinda wa Lilongwe.

MTTV
13/07/2026

Cancer iweyo ayi zikomo💔💔😭😭M'modzi mwa oyimba nyimbo za uzimu yemwe amadziwika kuti Enesia wamwalira akulandira thandizo...
11/07/2026

Cancer iweyo ayi zikomo💔💔😭😭

M'modzi mwa oyimba nyimbo za uzimu yemwe amadziwika kuti Enesia wamwalira akulandira thandizo la zaumoyo m'dziko la Canada.

Enesia amayimba nawo mu Chitheka(family) choir.

May her beautiful soul rest in peace.

MTTV
11/07/2026

11/07/2026

Nkhani ya nzibambo amene wauka kwa akufa patapita dzaka dzaka ali kumanda m'boma la Salima⚰️⚰️⚰️

MTTV
11/07/2026

11/07/2026

Finally awa ndi malo omaliza omwe Machine Bolo Young (Misheck Nkhoma) wagonapo mpakampa😭😭💔

Rest easy Bolo Young Machine🕊️🕊️🕊️

MTTV
11/07/2026

11/07/2026

Nkhani ya m'nyamata amene wangofikira Kumenyana ndi bambo ake akuchokera m'dziko la Africa.

MTTV
11/07/2026

Address

251 Pearl Street Laudium
Pretoria
0037

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Malawi Trends TV posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share