Halal Harmonies

Halal Harmonies Halal Harmonies, a premier Islamic record label dedicated to promoting faith-inspired melodies

05/08/2025

Nazrul Siraaj

30/07/2025

Uyuyu Nazrul Siraaj yi ineyo ndilibe naye zokamba 🔥🔥🔥👑🍂

"Exciting News!!! 🤩 We're beyond excited to announce that we've partnered with InkosiNation  for the Acappela Live Conce...
26/07/2025

"Exciting News!!! 🤩 We're beyond excited to announce that we've partnered with InkosiNation for the Acappela Live Concert! 🎵 Stay tuned for more details, as we can't wait to share this incredible experience with you. Get ready for an unforgettable Acappela Live concert! 🌙 "

14/06/2025

Nazrul Siraaj UYUYU
Ohooooo Kaya
🔥🔥🙌🙌
Chonena chagwela mkati

Pomwe chakachi chikumkela mkela mnyamata wanu Nazrul Siraaj wavumbulutsaso Video uku yomwe ikutchedwa Adalakwanji (Free ...
21/05/2025

Pomwe chakachi chikumkela mkela mnyamata wanu Nazrul Siraaj wavumbulutsaso Video uku yomwe ikutchedwa Adalakwanji (Free Palestine)

Taonelani inu
This guy is something else

@

A powerful and emotive nasheed by Nazrul Siraaj, calling for freedom and justice for palestine. With heartfelt Lyrics and soulful vocals, this song is poign...

Paja tinati tili ndi zolengezaTiyambe Motele ChakachiMfumu Nazrul Siraaj Ikudza ndi Nasheed title yake manthaTatiyeni ti...
12/05/2025

Paja tinati tili ndi zolengeza

Tiyambe Motele Chakachi
Mfumu Nazrul Siraaj Ikudza ndi Nasheed title yake mantha

Tatiyeni tidikile kuti muli zotani umumu

12/05/2025

Tili ndi zolengeza madzulowu

السلام عليكمMuli bwanjiPomwe tikadali busy ndi anyamata athu mu studioAs Halal Harmonies tili ndi nkhani zabwino zomwe t...
04/05/2025

السلام عليكم
Muli bwanji

Pomwe tikadali busy ndi anyamata athu mu studio

As Halal Harmonies tili ndi nkhani zabwino zomwe tikhale tikulengeza pamudzi pano, so aitaneni anzanuo abwele azazionele okha,
Pakali pano taonelani Nasheed imeneyi ya mama Aminah yomwe wapanga feature mnyamata wathu Nazrul Siraaj

Uyu ndi Chedyiya Yasin Jiah the poetAti akuphana maso ndi maso ndi Nazrul Siraaj mu project Yao yoyamba kuchokela ku Hal...
12/04/2025

Uyu ndi Chedyiya Yasin Jiah the poet
Ati akuphana maso ndi maso ndi Nazrul Siraaj mu project Yao yoyamba kuchokela ku Halal Harmonies

Heeee Zilikotu Ziliko

Artist Uyuyu amangoona kupangidwa Underrate Koma eeee ndinkhanizina ndipo Luso lake silokakamizaTaonela zomwe akupanga k...
01/04/2025

Artist Uyuyu amangoona kupangidwa Underrate Koma eeee ndinkhanizina ndipo Luso lake silokakamiza

Taonela zomwe akupanga ku Halal Harmonies Amalawi let's give him some flowers while we are waiting for something great something big from Nazrul Siraaj


Lero ndi Lachisanu Mesa Yasin Jiah Jumuah Mubarak
21/03/2025

Lero ndi Lachisanu Mesa Yasin Jiah
Jumuah Mubarak

Amfumu Che Nazrul SiraajKodi 2025 timuyamba motani ❓Stay Tuned
20/03/2025

Amfumu Che Nazrul Siraaj
Kodi 2025 timuyamba motani ❓

Stay Tuned

Address

4th Avenue
Pretoria
0001

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Halal Harmonies posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category