Afufuzi

Afufuzi This is a media platform for any form of entertainment such as music, poetry, sports, news and scandals.

25/06/2026

Anangoti ulowetse bwino kuli chilonda ine kuphwera kunali komweko πŸ™ŒπŸ˜­

25/06/2026

Zaziwika kuti anapha Chilima ndi Felix Njawala ndi Kaliati
πŸ’”πŸ˜­πŸ˜­πŸ˜­

24/06/2026

Kafukufuku wa ndenge ukuyenda bwanji?

Ibwerezenso by Caxy x Jay Jay Cee  ndi Nyimbo ya bwino kwambiriMwayionera kale?Iwe Dj Ibwerezenso πŸ”₯
13/04/2026

Ibwerezenso by Caxy x Jay Jay Cee ndi Nyimbo ya bwino kwambiri

Mwayionera kale?
Iwe Dj Ibwerezenso πŸ”₯

"Ibwelezenso" by Caxy x Jay Jay Cee is a high-energy party anthem that brings the heat to the dance floor. Let the fire blaze.This track is all about good vi...

Itatiphe ndi misonkho yomweyi.Komanso sugar wakwera.DPP woyeee! πŸ”₯
24/01/2026

Itatiphe ndi misonkho yomweyi.
Komanso sugar wakwera.

DPP woyeee! πŸ”₯

10/12/2025

let's vote

yodula or yosadula

08/12/2025

chonde amuna anga ku jonikoπŸ‡ΏπŸ‡¦ chonde muzivala condom ineso kuno sindikumalora opanda condomπŸ’”πŸ˜­πŸ˜­πŸ˜­ chonde chonde πŸ™πŸ™

08/12/2025

Mwana uyu wandikumbutsa Evison Matafale

22/11/2025

wina wamangidwa uku. Tikunena uyu mtsikana odziwika bwino ndi ma content yu.

21/11/2025

koma izi zikuchitakadi izi

Address

Pretoria

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Afufuzi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share