Mau amulungu

Mau amulungu Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Mau amulungu, Publisher, Soweto.

26/07/2024
Tiyeni tisiye tchito zakumidima thawi isanatithele 👌
07/05/2022

Tiyeni tisiye tchito zakumidima thawi isanatithele 👌

Pamene ochimwa akalowa m'manda anthu kudziko sadziwa zoomwe zikuchitika m'mandamo 🤷‍♂️. Zikufunika kulingalira mozama b4...
31/01/2022

Pamene ochimwa akalowa m'manda anthu kudziko sadziwa zoomwe zikuchitika m'mandamo 🤷‍♂️. Zikufunika kulingalira mozama b4 dead

21/01/2020

Nthaw ya nowa Anthu ankawuzidwa k*ti kubwera mvura yadzaoneni tiyeni tiseme chombo, koma anthu ankayesa ngat nthabwala nayamba kumunyogodola nowa nkumat wakalamba, koma nowa sanasamale zokamba zawanthu koma kupitiliza kusema chombo, atamaliza kusema chombo chinja yekha ndi anthu ena ochepa mwaiyo,. Nowa anawakakamizabe Anthu omwe anakana kusema chombo chinja k*ti akuyenera kulowa m'mchombo muja, koma anthu anakanilatu kwaantuwagalu ndipo nowa analowa m'mchombo muja ndiyaanthu ochepa komanso ziweto, kenako patangotha mphindi zochepa chitseko chinasekeka choka mvula nayamba kugwa mosalekeza ndipo anthu anagogoda pankhomo la chombo chinja k*t nowa atsekule koma nowa anawayakha anthu aja k*t siine amene ndatseka, pamapeto pake anthu onse anafa.

Ndiye ndichimodzimodzi masiku ano kumva tilikumva koma tikuzengeleza kulapa mchimo lomwe tilinalo m'muntima mwanthu koma sitikufuna kusiya ndikulapa, koma dziwa chitsilu ndiamene amamva mau amulungu koma osawasamala. TIYENI TILAPE MCHIMO LANTHU MWANSANGA PAMENO NTHAWI IKADALIPO UKAMWAL IRA LERO UTALAPA MCHIMO LAKO MULUNGU AMAKONDWERA PAKUTI MALEMBA AMATI MULUNGU SAKONDWERA NDIIFA YAWOCHIMWA

AMEN

Olalika alikularikabe ndipo iwe ukadalibe ndimoyo koma sukufuna kulapa, koma dziwa odala ndiomwe amamva mau amulungu ndi...
21/01/2020

Olalika alikularikabe ndipo iwe ukadalibe ndimoyo koma sukufuna kulapa, koma dziwa odala ndiomwe amamva mau amulungu ndikuwachita

Never boast about tomorrow.You don't know what will happen between now and then!!!!!
28/09/2019

Never boast about tomorrow.You don't know what will happen between now and then!!!!!

lets be trust in Almighty God,so that we 'll see his glory.
31/05/2019

lets be trust in Almighty God,so that we 'll see his glory.

Moni anthu amulungu omwe muli m'gululi komanso amene asali mugululi ndipepha mulungu wamwambayo akudalitseni konse komwe...
10/05/2019

Moni anthu amulungu omwe muli m'gululi komanso amene asali mugululi ndipepha mulungu wamwambayo akudalitseni konse komwe muli.

NDAFUNA KUKUTSIWITSANI KUTI TSIKU LALERO KULI UNTHENGA WABWINO WAMULUNGU WAMWAMBAYO OMWE TINGAGAWANE INU NDI INE USIKU UNO CHONDE NDIKUKUPEPHANI NONSE AMENE MUMAKONDA ULALIKI KUTI MUKHALE MULI ONLINE (TIME 7:30).

Address

Soweto

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mau amulungu posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category