20/10/2025
Not_football_related
Chidziwitso; president yemwe wangosankhidwa mwezi wapitawu ku Malawi prof.. A. Peter Mutharika, wayankhura ku mtundu wa amalawi onse dzuro Kwa Chonde komwe kumachitika mwambo wa chikhalidwe Cha alhomwe (mulhakho wa alhomwe) k*ti "kuyambira January chaka Cha mawa sukulu za Secondary komanso za primary zonse zomwe zili za boma, zizakhala za ulele (free fees) ndipo wachenjeza makolo onse k*ti kuyambira January chaka Cha mawa sakufuna kuona mwana pakhomo nthawi ya maphunziro chifukwa zomwe makolo manamizira mmbuyomu k*t ndalama yolipilira mwana ku sukulu alibe pano yachotsedwa ndipo azisowa chonamizira.
Makolo osunga ana pakhomo nthawi ya maphunziro azathana nawo
Video will follow