Halal Harmonies

Halal Harmonies Halal Harmonies, a premier Islamic record label dedicated to promoting faith-inspired melodies

14/06/2025

Nazrul Siraaj UYUYU
Ohooooo Kaya
🔥🔥🙌🙌
Chonena chagwela mkati

Pomwe chakachi chikumkela mkela mnyamata wanu Nazrul Siraaj wavumbulutsaso Video uku yomwe ikutchedwa Adalakwanji (Free ...
21/05/2025

Pomwe chakachi chikumkela mkela mnyamata wanu Nazrul Siraaj wavumbulutsaso Video uku yomwe ikutchedwa Adalakwanji (Free Palestine)

Taonelani inu
This guy is something else

@

A powerful and emotive nasheed by Nazrul Siraaj, calling for freedom and justice for palestine. With heartfelt Lyrics and soulful vocals, this song is poign...

Paja tinati tili ndi zolengezaTiyambe Motele ChakachiMfumu Nazrul Siraaj Ikudza ndi Nasheed title yake manthaTatiyeni ti...
12/05/2025

Paja tinati tili ndi zolengeza

Tiyambe Motele Chakachi
Mfumu Nazrul Siraaj Ikudza ndi Nasheed title yake mantha

Tatiyeni tidikile kuti muli zotani umumu

12/05/2025

Tili ndi zolengeza madzulowu

السلام عليكمMuli bwanjiPomwe tikadali busy ndi anyamata athu mu studioAs Halal Harmonies tili ndi nkhani zabwino zomwe t...
04/05/2025

السلام عليكم
Muli bwanji

Pomwe tikadali busy ndi anyamata athu mu studio

As Halal Harmonies tili ndi nkhani zabwino zomwe tikhale tikulengeza pamudzi pano, so aitaneni anzanuo abwele azazionele okha,
Pakali pano taonelani Nasheed imeneyi ya mama Aminah yomwe wapanga feature mnyamata wathu Nazrul Siraaj

Uyu ndi Chedyiya Yasin Jiah the poetAti akuphana maso ndi maso ndi Nazrul Siraaj mu project Yao yoyamba kuchokela ku Hal...
12/04/2025

Uyu ndi Chedyiya Yasin Jiah the poet
Ati akuphana maso ndi maso ndi Nazrul Siraaj mu project Yao yoyamba kuchokela ku Halal Harmonies

Heeee Zilikotu Ziliko

Artist Uyuyu amangoona kupangidwa Underrate Koma eeee ndinkhanizina ndipo Luso lake silokakamizaTaonela zomwe akupanga k...
01/04/2025

Artist Uyuyu amangoona kupangidwa Underrate Koma eeee ndinkhanizina ndipo Luso lake silokakamiza

Taonela zomwe akupanga ku Halal Harmonies Amalawi let's give him some flowers while we are waiting for something great something big from Nazrul Siraaj


Lero ndi Lachisanu Mesa Yasin Jiah Jumuah Mubarak
21/03/2025

Lero ndi Lachisanu Mesa Yasin Jiah
Jumuah Mubarak

Amfumu Che Nazrul SiraajKodi 2025 timuyamba motani ❓Stay Tuned
20/03/2025

Amfumu Che Nazrul Siraaj
Kodi 2025 timuyamba motani ❓

Stay Tuned

السلام عليكم ورحمة الله وبركاته Ndife okondwa kukudziwitsani kuti tapanga Sign Yasin Jiah ngati mmodzi mwa Ma artist ath...
17/03/2025

السلام عليكم ورحمة الله وبركاته
Ndife okondwa kukudziwitsani kuti tapanga Sign Yasin Jiah ngati mmodzi mwa Ma artist athu a Halal Harmonies

Yasin Jiah ndi wachiwili kupangidwa sign ku Halal Harmonies pambuyo poti tinapanga sign Nazrul Siraaj

Zabwino zikumka nabwelabe

16/03/2025

Tibwelaso ndi zolengeza Zina posachedwapa
🤗🤗🤗🤗

"BIG NEWS!We're thrilled to announce that we've signed the incredibly talented Nazrul Siraaj  as our FIRST ARTIST of Hal...
15/03/2025

"BIG NEWS!

We're thrilled to announce that we've signed the incredibly talented Nazrul Siraaj as our FIRST ARTIST of Halal Harmonies!

Get ready for some soul-stirring Nasheeds and inspiring melodies that will uplift your spirits!

Stay tuned for upcoming releases, behind-the-scenes insights, and exclusive updates from Nazrul Siraaj and Halal Harmonies!

🤗🤗✨

"

Address

Thulamahashe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Halal Harmonies posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category