16/03/2024
Lyrics of Pusha by Starpie Mukatha
Kodi ase,ndimafunatu mundigailekotu kadolla kenakaketu ase.
Eeh panopatu ndembolatu,sindikulimbatu kudeni kwanuko dzulo.
Eeh panopatu.
Ndikudziwa gamuyi yakukulila.
Kuchitakusowa mtengoogwila.
Achibale kumbaliakuyanganila,akuyanganilaaaaah.
Komadziwaaah,ukachuluka,mdima,kwasalapang'onokucha aaah.
Zizayenda,zizayenda.
Limbikabe,limbikabe.
Usafooke,usafooke.
Ponyelakwakuya,ponyelakwakuya.
Phusha,usagwelemphwayi.
Ukanalinawomwayi,uthakuyesakachikena,kachikena,kena.
Usamachedwekutiakugwilemkono.
Ukuchedwauzanongonezabondo.
Malomokuthandiza,azakupasankhonyo,dzakupasankhonyo.
Ubater push hard work hard everyday.
Lo
Wanipaliposemani ngati venda.
Sikadzakokhaaa kaopa kulaula,kaopa kulaula.
Succes imabwela ukalimbika,imabwela,ukalimbika.
Ndeno fada pusha,phusha pusha,pusha ndati fadapusha.
Phusha,usagwele mphwayi.
Ukanalinawomwayi.
Uthakuyesa kachikena kachikena kena