Zonse TV

Zonse TV Welcome to Zonse TV! PANO TIMAPANGA SHARE NKHANI ZOSIYANASIYANA ZOMWE ANTHU ZAWACHITIKIRA .
(2)

NKHANI ZILIZONSEZO TIMAPANGA SHARE.This is your story, your laughter, your reality. ZSTV- Everything-For Everyone.📺🎥
Tumizani nkhani zanu pompano pa Zonse TV💚

KOMA NDALAMA 🤣🇲🇼 Zonse TV
22/07/2025

KOMA NDALAMA 🤣

🇲🇼 Zonse TV

22/07/2025

In Iran, three people robbed a jewelry showroom and killed the owner💔

The government hanged them in front of the shop. Justice within 15 days....

🇮🇷 Zonse TV 🇲🇼

A Mikozi akutelotu kuseliku...Nanga Inu muti bwanji 🇲🇼 Zonse TV 💚
21/07/2025

A Mikozi akutelotu kuseliku...
Nanga Inu muti bwanji

🇲🇼 Zonse TV 💚

NDIYE MWATI CHILD BIRTH COMPETITION? 🙄Pangani FOLLOW apa👉 Zonse TV  kuti timve zambiri.
20/07/2025

NDIYE MWATI CHILD BIRTH COMPETITION? 🙄

Pangani FOLLOW apa👉 Zonse TV kuti timve zambiri.

MASAMU AVUTA PA GROUND LA Dr. LAZ😊😊
20/07/2025

MASAMU AVUTA PA GROUND LA Dr. LAZ😊😊

His Ex-cellency Dr. LAZ CHAKWERA WANENETSA KUTI“Mukandivoteranso, palibe atakhale lova”Pomwe Makolo akale adati ukanama ...
20/07/2025

His Ex-cellency Dr. LAZ CHAKWERA WANENETSA KUTI
“Mukandivoteranso, palibe atakhale lova”

Pomwe Makolo akale adati ukanama sikuchedwa kucha, mwambiwu ku nyumba ya chifumu sukuwatekesa. Chitadzodza matope achinyamata pa nkhani yowathetsera ulova, chipani cha MCP motsogozedwa ndi mtsogoleri wake Lazarus Chakwera chati chikangowina chisankho ulendo uno, ulova mdziko muno ikhala nkhani ya make dzana.

The Best GOSPEL Artist in Malawi..🇲🇼🔥🔥
20/07/2025

The Best GOSPEL Artist in Malawi..🇲🇼🔥🔥

20/07/2025

Basitu akuti Boma ndi lomweli chifukwa Cha ka K500,000

04/07/2025

KUBA KWANJI UKU DZUWA LILI NG'EEE👽

02/07/2025

ABEG OOO ...MUKUTI ZAKHALA BWANJI NAWO MA NAIJA WA...

Moni Moni Moni kulikonse komwe Muli....Nanga muli bwanji lero...Osaiwala kupanga share nkhani zanu ,zoseketsa, za malodz...
11/06/2025

Moni Moni Moni kulikonse komwe Muli....Nanga muli bwanji lero...

Osaiwala kupanga share nkhani zanu ,zoseketsa, za malodza, zokhumudwitsa, zosangalatsa kapena zolangiza tiye nazoni pompano pa Zonse TV kuti timve zomwe zikukuchitikirani mmadera osiyanasiyana.....

💔💔💔------------------------------Inu AZIMAYI Ena akufunsa uku kuti;  Kodi mkazi yemwe mamuna wake amangokhalira kudandau...
10/06/2025

💔💔💔
------------------------------
Inu AZIMAYI Ena akufunsa uku kuti; Kodi mkazi yemwe mamuna wake amangokhalira kudandaula kuti chakudya sichili bwino nthawi zonse mmatani,? kapena MUNGAMUTHANDIZE bwanji yemwe akudutsa munyengo zoterezi chifukwa awa amuna awo sakuwayankha zolungosoka akafunsa chomwe sichili bwino muchakudya mo!??🥲

©
Follow Zonse TV by just clicking here 👉 Zonse TV and Share your stories or your concerns.

Address


Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Zonse TV posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

  • Address
  • Alerts
  • Contact The Business
  • Want your business to be the top-listed Media Company?

Share