Zimbabwe Chewa Nyanja News

Zimbabwe Chewa Nyanja News Mverani nkhani zadziko lathu laZimbabwe ndizina zochokera kumayiko ena muChichewa...

Madotolo akuMpilo Hospital muboma laBulawayo, akwanitsa kutchotsa chotupa mmimba yamai wina wazaka 32 ochokera kuMbereng...
14/11/2025

Madotolo akuMpilo Hospital muboma laBulawayo, akwanitsa kutchotsa chotupa mmimba yamai wina wazaka 32 ochokera kuMberengwa. Ichi ndichi zindikiro chaluso lapamwamba. A Ms Melody Ndlovu, anakala zaka zisanu muululu wachotupacho. Chotupacho china lemera 50kg ndipo chima sokoneza ntchitho zamai Ndlovu. ANdlovu akupeza bwino chifukwa operation ina yenda bwino.

Kwagwa mpungwe pungwe mudziko laTanzania pamene anthu okwiya akupanga zionetsero chifukwa chazisankho.  Mutsogoleri wa d...
30/10/2025

Kwagwa mpungwe pungwe mudziko laTanzania pamene anthu okwiya akupanga zionetsero chifukwa chazisankho. Mutsogoleri wa dziko laTanzania amai Samia Suluhu Hassan akuimaso pazisankozo zimene otsutsa boma sakuima nawo kamba komangidwa ndikuzunzidwa ndiapolisi. Izi zikuonetsa kuthi President Samia Hassan akuimila zisanko payekha zimene zakwiyisa nzika zadziko laTanzania. Apolisi akwetsa utsi waTeargas ndikumanga anthu mumzinda waukhulu Dar Es Salaam. Boma lakazikitsa Curfew kuyambila 6pm madzulo mpakana 6am mamawa. Dziko laTanzania lina kwanitsira kukkweza chuma chadziko ndi 5.5% chaka chatha ndiposo mtsogoleri anayambitsa zithukuko zingapho mdzikoli. President Hasaan anakwexedwa paudindo muchaka cha2021 pamene anali Vice President. Anatenga udindo waPresident kutsatira imfa ya aJohn Magufuli mu2021.

Boma laZimbabwe lapeleka chithandizo chamankhwala a Anti Retroviral ku Boma laBotswana.  Pa 29 October 2025 galimoto lon...
30/10/2025

Boma laZimbabwe lapeleka chithandizo chamankhwala a Anti Retroviral ku Boma laBotswana. Pa 29 October 2025 galimoto lonyamula mankwalawa lanyamuka kuchokera kudziko laZimbabwe wakuBotswana. 80% yamankwala idzakala ngongole pamene 20% idzakala chithandizo. Olemekezeka amai Sarah Sarah S. Molosiwa Ambassador wadziko laBotswana kuZimbabwe anakala nawo pamwambo wonyamula mankwalawo pamodzi ndi oyimira NATPHARM company yamankwalawo ndiena oyimira boma laZimbabwe..

Tiyeni tiyeni kumaGems..Alunta Continua...
25/10/2025

Tiyeni tiyeni kumaGems..Alunta Continua...

25/10/2025
22/10/2025
Aphungu anyumba yamalamuro muZimbabwe adandaula kwambiri ndimmene akuzunzika ndiumoyo masiku onse.  Phungu wa dera la Dz...
22/10/2025

Aphungu anyumba yamalamuro muZimbabwe adandaula kwambiri ndimmene akuzunzika ndiumoyo masiku onse. Phungu wa dera la Dzivarasekwa olemekezeka aEdwin Mushora, anena kuthi anakuzidwa kwambiri ndi imfa yaphungu waku Nkulumane, Bulawayo olemekezeka malemu Desire Moyo omwe ana mwalira pangozi ya galimoto mumsewu waukhulu pomwe galimoto yomwe anakwera inawombana ndi Njovu. Olemekezeka aMushora athi izi zinadza chifukwa chosa pasidwa mafuta oyendetsa galimoto amene aphungu amawa peza kuchokera ku boma (Fuel allowance). AMushora anenes kuthi aphungu akukhala momvetsa chisoni ndiye apempha boma laPresident Mnangagwa kuthi lichitepo kanthu.

22/10/2025

Boma laEthiopia, lalengeza kuthi onse anthu amene anapasidwa kapena adzapasidwa Honorary Doctorate Degree mumaUniversity amdzikolo asagwirise ntchito dzina lothi Doctor. Lathiso anthu ogwira nchitho mmboma saza loledwa kupasidwa maHonorary Degree pokha akatuluka muntchito zaboma..

https://www.facebook.com/share/v/1KDTTQhyBt/

Dziko laChina lalengeza kuthi lidza chotsa ngongole yomwe dziko laMalawi lida thenga.  Ngongoleyo ndiyo kwanila $20 mili...
21/10/2025

Dziko laChina lalengeza kuthi lidza chotsa ngongole yomwe dziko laMalawi lida thenga. Ngongoleyo ndiyo kwanila $20 miliion imene iliK35Billion yaMalawi.

Chipani cholamulira chaZANU PF chagwirizana kuthi mtsogoleri wadziko oremekeza President Emmerson Mnangagwa apitirize ul...
21/10/2025

Chipani cholamulira chaZANU PF chagwirizana kuthi mtsogoleri wadziko oremekeza President Emmerson Mnangagwa apitirize ulamuliro wadziko mpaka chaka cha2030. Izi ana lengeza pamkhumano wawu kulu omwe unachitikira ku boma laMutare. Povomereza ndondomeko iyi, anthu achipani chaZanu PF atsimikiza kuthi ndizofunikira kuthi utsogoleri wa aMnangagwa upitirize kutukula dziko laZimbabwe.

Anthu makumi atathu ndiasanu ndimmodzi omwe anamwalira pangozi yabhasi kuLimpopo ndiakuZimbabwe.  nthambi yofufuza yaFor...
21/10/2025

Anthu makumi atathu ndiasanu ndimmodzi omwe anamwalira pangozi yabhasi kuLimpopo ndiakuZimbabwe. nthambi yofufuza yaForensic Investigation yanena izi kutsatila kufufuza kumene anapanga iwowo pofuna kudziwa anthu omwe ana thaya miyoyo yawo pangozi imeneyi. Tilira limodzi ndima banja
okudzidwa.

Antu makumi anai ndimmodzi akuganiziridwa kuthi amwalira pangozi yabhasi yochokera kuSouth Africa paulendo wakuMalawi vi...
13/10/2025

Antu makumi anai ndimmodzi akuganiziridwa kuthi amwalira pangozi yabhasi yochokera kuSouth Africa paulendo wakuMalawi via Zimbabwe...munali anthu akuZimbabwe ni aMalawi.

Address

Bulawayo

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Zimbabwe Chewa Nyanja News posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share